TextSongAI

WHY

Male golden alto vocalpure malawian chichewa accentSouth African amapianolong drum112BPM

Created by: TextSongAI

Created: Sep 23, 2026

Duration: 4:55

[Intro]

Oh yeah...
Mmm yeah...
Moyo ndi wodabwitsa...
Nthawi zina timangofunsa...

Why?

[Verse 1]

Umanena kuti umandikonda, chifukwa  chani  koma
Umaseka ndikamalira, chifukwa chani koma
Unasintha utalonjeza, chifukwa chani koma
Umathawa ukafunidwa, chifukwa chani koma

Wina makupatsa love iwe mamupatsa pain
Wina amakukhulupirira, iwe umamuphwanyira mtima
Ukaona mnzako akuvutika, umangodutsa 
Pamene uli ndi zambiri, n'chifukwa chiyani sugawana

[bridge]

Timalota chikondi, koma timabzala ululu,
Timalota mtendere, koma timabzala ndewu,
Tili ndi chowonadi, koma timasankha mabodza,
Nde moyo umakhala, chithunzi chosamveka...
Chifukwa chani, hey hey, chifukwa chani koma


[Chorus]

[Lead Vocalist]
Why, why, why, why, why?

[Call & Response]
N'chifukwa chiyani timachita zimenezi?

[Lead Vocalist]
Why, why, why, why, why?

[Call & Response]
N'chifukwa chiyani timapwetekana?

[Lead Vocalist]
Hey, hey, hey, hey, hey, hey!

[All]
Ooh yeah... palibe amene akudziwa!

[Verse 2]

Wina amasankha mtendere, wina amasankha ndewu why?
Wina amapereka chikondi, wina amachibisa why?
Wina akalandira zabwino, amaiwala amene anampatsa why?
Wina akalakwitsa, amadziwa koma sabwerera why?
Nthawi zina timakonda amene amatipweteka why?
Nthawi zina timasiya amene amatimvetsa why?
Timadziwa chabwino, koma timasankha cholakwika why?
Timafuna mtendere, koma timayamba ndewu why?

[Bridge]

Timalota chikondi, koma timabzala ululu,
Timalota mtendere, koma timabzala ndewu,
Tili ndi chowonadi, koma timasankha mabodza,
Nde moyo umakhala, chithunzi chosamveka...
Chifukwa chani hey hey, chifukwa chani koma

[Chorus]

[Lead Vocalist]
Why, why, why, why, why?

[Call & Response]
N'chifukwa chiyani timachita zimenezi?

[Lead Vocalist]
Why, why, why, why, why?

[Call & Response]
N'chifukwa chiyani timapwetekana?

[Lead Vocalist]
Hey, hey, hey, hey, hey, hey!

[All]
Ooh yeah... palibe amene akudziwa!

[Dance Break]

Why... why... why...
Moyo ndi wodabwitsa...

Why... why... why...
Tiyeni tivine...

Hey!
Hey!
Why?

[Final Chorus]

[Lead Vocalist]
Why, why, why, why, why?

[Call & Response]
N'chifukwa chiyani timakondana?

[Lead Vocalist]
Why, why, why, why, why?

[Call & Response]
N'chifukwa chiyani timapwetekana?

[Lead Vocalist]
Hey, hey, hey, hey, hey, hey!

[All]
Ooh yeah... palibe amene akudziwa!

[Lead Vocalist]
Why... why... why...

[All]
Why... why... why...

[Outro]

Moyo uli ndi mafunso...

Koma tiyeni tisangalale...

Why?

Oh yeah...
Why?

Create Your Own AI Music

Generate studio-quality songs in seconds

Get Started